TIMABUKU TOTHANDIZA ANTHU KUTIDZIWA BWINO PADZIKO LONSE
A Mboni za Yehova amayesetsa kutsatira mfundo za m’Baibulo zomwe zimathandiza kuti mabanja awo azikhala osangalala. Makolo a Mboni amaona kuti ali ndi udindo waukulu wophunzitsa ana awo mfundo za m’Baibulo.

