Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woimira Nthambi wa 2025-2026
‘Imvani Zimene Mzimu Ukunena ku Mipingo’
Pulogalamu yosonyeza chigawo cha m’mawa ndi masana cha msonkhano wadera wokhala ndi woimira nthambi.
Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
Mafunsowa adzayankhidwa pamsonkhanowu.