Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2024 Wakuti ‘Lalikirani Uthenga Wabwino’
Lachisanu
Pulogalamu ya lachisanu yachokera pa Luka 2:10—“Uthenga wabwino wa chimwemwe chachikulu chimene anthu onse adzakhale nacho.”
Loweruka
Pulogalamu ya Loweruka yachokera pa Salimo 96:2—“Tsiku ndi tsiku muzilengeza uthenga wabwino wa chipulumutso chake.”
Lamlungu
Pulogalamu ya Lamlungu yachokera pa Mateyu 24:14—“. . . kenako mapeto adzafika.”
Mawu kwa Osonkhana
Mfundo zothandiza amene asonkhana.
Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi
ZOKHUDZA IFEYO
Dzabwereni ku Msonkhano wa 2026—“Chimwemwe Chosatha”
Tikukuitanirani ku Msonkhano wa masiku atatu wachaka chino wa Mboni za Yehova.
MISONKHANO IKULUIKULU
Mukuitanidwa ku Msonkhano wa Mboni za Yehova wa 2024 Wakuti ‘Lalikirani Uthenga Wabwino’
Tikukuitanani kuti mudzakhale nafe pamsonkhano wa Mboni za Yehova wa masiku atatu wachaka chino.
MISONKHANO IKULUIKULU
Zimene Zili Muvidiyo Yakuti: Kuwala Kwenikweni kwa Dziko
Onerani zimene zili muvidiyo yoyamba yakuti Moyo wa Yesu Komanso Utumiki Wake. Vidiyo imeneyi idzaonetsedwa pamsonkhano wa 2024.

