Pulogalamu ya Msonkhano wa 2020
Pulogalamu ya Msonkhano wa Mboni za Yehova wa 2020 wakuti, ‘Kondwerani Nthawi Zonse.’
Lachisanu
Pulogalamu ya Lachisanu yachokera pa Afilipi 4:4—“Nthawi zonse kondwerani mwa Ambuye. Ndibwerezanso, Kondwerani.”
Loweruka
Pulogalamu ya Loweruka yachokera pa Salimo 105:3—“Nyadirani dzina lake loyera. Mtima wa anthu ofunafuna Yehova usangalale.”
Lamlungu
Pulogalamu ya Lamlungu yachokera pa Salimo 37:4—“Sangalala mwa Yehova, ndipo adzakupatsa zokhumba za mtima wako.”
Mawu kwa Osonkhana
Mawu othandiza anthu amene abwera pamsonkhano.

