Pulogalamu ya Msonkhano Wadera wa 2017-2018—Womwe Padzakhale Woimira Nthambi
Onani pulogalamu ya msonkhano waderawu, ilinso ndi nkhani zimene woimira nthambi adzakambe.
Musaleke Kukwaniritsa Chilamulo cha Khristu
Msonkhanowu udzafotokoza zimene chilamulo cha Khristu chimatanthauza komanso kuti tingachikwaniritse bwanji.
Muzimvetsera Mwachidwi Kuti Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
Mafunso amenewa adzayankhidwa pa msonkhano waderawu.

