Pulogalamu ya Msonkhano wa 2025 Wakuti ”Kulambira Koyera”

Lachisanu

Pulogalamu ya Lachisanu yachokera pa Mateyu 4:10​—“Yehova Mulungu wako ndi amene uyenera kumulambira.”

Loweruka

Pulogalamu ya Loweruka yachokera pa Yohane 2:17​—“Kudzipereka kwanga panyumba yanu kudzakhala ngati moto umene ukuyaka mumtima mwanga.”

Lamlungu

Pulogalamu ya Lamlungu yachokera pa Yohane 4:23​—“Adzalambira Atate motsogoleredwa ndi mzimu ndi choonadi.”

Mawu kwa Osonkhana

Mawu othandiza anthu amene asonkhana.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

ZOKHUDZA IFEYO

Dzabwereni ku Msonkhano wa 2026​​—⁠“Chimwemwe Chosatha”

Tikukuitanirani ku Msonkhano wa masiku atatu wachaka chino wa Mboni za Yehova.

MISONKHANO IKULUIKULU

Tikukuitanirani Kumsonkhano wa Mboni za Yehova wa 2025 wa Mutu Wakuti: “Kulambira Koyera”

Kodi Yesu anaphunzitsa zotani zokhudza kulambira koona?

MISONKHANO IKULUIKULU

Zimene Zili Muvidiyo Yakuti: Uthenga Wabwino wa Yesu: Gawo 2 ndi 3

Tsopano Yesu wakula ndipo wayamba kusonkhanitsa ophunzira ake. Komabe, anthu ayamba kale kumutsutsa pa utumiki wake.