Egypt

 

2017-09-21

EGYPT

‘Ndikufunitsitsa Kudzaona Boma Litachotsa Chiletso Chomwe Linaikira a Mboni za Yehova’

Zaka zambirimbiri m’mbuyomo, a Mboni za Yehova ankapembedza mwaufulu ku Egypt. Nyuzi ina ya paintaneti inafotokoza kuti kuchokera nthawi imeneyo a Mboni za Yehova akhala akusonyeza makhalidwe abwino ngakhale kuti akhala akuzunzidwa kwa zaka zambiri.