Tsiku Loyamba
“Yehova Mulungu wako ndi amene uyenela kumulambila”—Mateyo 4:10
M’mawa
-
8:20 Vidiyo ya Nyimbo
-
8:30 Nyimbo Na. 74 ndi Pemphelo
-
8:40 NKHANI YA CHEYAMANI: Kodi Kulambila Koyela N’ciyani? (Yesaya 48:17; Malaki 3:16)
-
9:10 SEWELO LALIKULU LA M’BAIBO:
Mbili ya Umoyo wa Yesu: Gawo 2
“Uyu Ndiye Mwana Wanga”—Mbali 1 (Mateyo 3:1–4:11; Maliko 1:12, 13; Luka 3:1–4:7; Yohane 1:7, 8)
-
9:40 Nyimbo Na. 122 ndi Zilengezo
-
9:50 YOSIYILANA: Maulosi Onena za Mesiya Anakwanilitsika!—Gawo 1
-
• Anavomelezedwa ndi Mulungu (Salimo 2:7; Mateyo 3:16, 17; Machitidwe 13:33, 34)
-
• Anacokela m’Banja la Mfumu Davide (2 Samueli 7:12, 13; Mateyo 1:1, 2, 6)
-
• Anadzozedwa Kukhala “Mesiya Mtsogoleli” (Danieli 9:25; Luka 3:1, 2, 21-23)
-
-
10:45 Ndani Makamaka Amene Akulamulila Dziko? (Maliko 12:17; Luka 4:5-8; Yohane 18:36)
-
11:15 Nyimbo Na. 22 ndi Kupumula
Masana
-
12:35 Vidiyo ya Nyimbo
-
12:45 Nyimbo Na. 121
-
12:50 YOSIYILANA: Tengelani Mmene Yesu Anayankhila Woyesayo!
-
• Khalani ndi Moyo mwa Mawu a Yehova (Mateyo 4:1-4)
-
• Musamuyese Yehova (Mateyo 4:5-7)
-
• Lambilani Yehova Yekha (Mateyo 4:10; Luka 4:5-7)
-
• Muzicikhalila Kumbuyo Coonadi (1 Petulo 3:15)
-
-
13:50 Nyimbo Na. 97 ndi Zilengezo
-
14:00 YOSIYILANA: Zimene Tingaphunzilepo Tikadziwa Bwino Malo a m’Nthawi ya Yesu
-
• Cipululu ca Yudeya (Mateyo 3:1-4; Luka 4:1)
-
• Cigwa ca Yorodano (Mateyo 3:13-15; Yohane 1:27, 30)
-
• Yerusalemu (Mateyo 23:37, 38)
-
• Samariya (Yohane 4:7-9, 40-42)
-
• Galileya (Mateyo 13:54-57)
-
• Foinike (Luka 4:25, 26)
-
• Siriya (Luka 4:27)
-
-
15:10 Kodi Yesu Amaonamo Ciyani Mwa Inu? (Yohane 2:25)
-
15:45 Nyimbo Na. 34 ndi Pemphelo Lothela

