Tsiku Lacitatu
“Adzalambila Atate motsogoleledwa ndi mzimu ndi coonadi”—Yohane 4:23
M’mawa
-
8:20 Vidiyo ya Nyimbo
-
8:30 Nyimbo Na. 140 ndi Pemphelo
-
8:40 YOSIYILANA: Zimene Tingaphunzilepo pa Mawu Amene Yesu Anakamba
-
• “Kubadwa mwa Madzi ndi Mzimu” (Yohane 3:3, 5)
-
• “Palibe Munthu Amene Anakwelapo Kumwamba” (Yohane 3:13)
-
• ‘Fikani Pamene Pali Kuwala’ (Yohane 3:19-21)
-
• “Munthu Ameneyo ndi Ineyo” (Yohane 4:25, 26)
-
• “Cakudya Canga” (Yohane 4:34)
-
• “M’mindamo . . . Mwayela Kale Ndipo M’mofunika Kukolola” (Yohane 4:35)
-
-
10:05 Nyimbo Na. 37 ndi Zilengezo
-
10:15 NKHANI YA ANTHU ONSE: Kodi Mumacidziwa Cimene Mumalambila? (Yohane 4:20-24)
-
10:45 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
-
11:15 Nyimbo Na. 84 ndi Kupumula
Masana
-
12:35 Vidiyo ya Nyimbo
-
12:45 Nyimbo Na. 77
-
12:50 SEWELO LALIKULU LA M’BAIBO:
Mbili ya Umoyo wa Yesu: Gawo 3
“Ndine Amene” (Yohane 3:1–4:54; Mateyo 4:12-20; Maliko 1:19, 20; Luka 4:16–5:11)
-
13:35 Nyimbo Na. 20 ndi Zilengezo
-
13:45 Kodi Mwaphunzila Ciyani?
-
13:55 Khalanibe m’Kacisi Wamkulu Wauzimu wa Yehova! (Aheberi 10:21-25; 13:15, 16; 1 Petulo 1:14-16; 2:21)
-
14:45 Nyimbo Yatsopano Komanso Pemphelo Lothela

