Pulogilamu ya Msonkhano wa 2025 wa Mutu Wakuti Kulambila Koyela
Tsiku Loyamba
Pulogilamu ya tsiku loyamba lacokela pa Mateyo 4:10—“Yehova Mulungu wako ndi amene uyenela kumulambila.”
Tsiku Laciwili
Pulogilamu ya tsiku laciwili latengedwa pa Yohane 2:17—“Kudzipeleka kwanga panyumba yanu kudzakhala ngati moto umene ukuyaka mumtima mwanga.”
Tsiku Lacitatu
Pulogilamu ya tsiku lacitatu yacokela pa Yohane 4:23—“[Lambilani] Atate motsogoleledwa ndi mzimu ndi coonadi.”
Mawu kwa Osonkhana
malangizo othandiza kwa opezeka pa msonkhano
Mungakondenso Izi
ZOKHUDZA IFE MBONI
Misonkhano Ikuluikulu ya Mboni za Yehova
Anthu onse ndi olandilidwa ku misonkhano yaulele ya pacaka imeneyi.
MISONKHANO IKULUIKULU
Tikukuitanilani ku Msonkhano Wacigawo wa Mboni za Yehova wa 2025 wa Mutu Wakuti “Kulambila Koyela”
Kodi Yesu anaphunzitsa ciyani pa nkhani ya kulambila koona?
MISONKHANO IKULUIKULU
Kadyonkho ka Sewelo Lalikulu la m’Baibo Lakuti: Mbili ya Umoyo wa Yesu: Gawo 2 ndi 3
Tsopano Yesu wakula ndipo wayamba kusonkhanitsa ophunzila ake. Komabe, posacedwa ayamba kutsutsidwa mu utumiki wake.

