Gao 3: “Ndine Amene”
Yesu akudzidziwikitsa kwa anthu ambili kuti ndiyedi Mesiya ndipo ena akumukhulupilila, koma ena sakukhulupilila. Mogwilizana ndi Yohane 3:1-36; Maliko 6:17-20; Mateyu 14:3-5; Luka 3:19, 20; Yohane 4:1-45; Maliko 1:14, 15; Mateyu 4:17; Luka 4:14, 15; Yohane 4:46-54; Luka 4:16-30; Mateyu 4:13-16; Luka 5:1-11; Mateyu 4:18-22; Maliko 1:16-20.

