Kodi zimene Yesu anaphunzitsa n’zothandiza masiku ano?

Kodi Zimene Yesu Anaphunzitsa N’zothandiza Masiku Ano?

Cinyanja
Kodi Zimene Yesu Anaphunzitsa N’zothandiza Masiku Ano?
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102024309/univ/art/1102024309_univ_sqr_xl.jpg
T-jss masa. 1-2

Kodi zimene Yesu anaphunzitsa n’zothandiza masiku ano?

Kodi zimene Yesu anaphunzitsa n’zothandiza masiku ano?

“Zinthu zonse zimene mumafuna kuti anthu akucitileni, inunso muwacitile zomwezo.”​Mateyo 7:12.

Yesu anaphunzitsanso kuti

Onelelani vidiyo yakuti, Mbili ya Umoyo wa Yesu pa jw.org.