“Aliyense wa inu azikonda mkazi wake ngati mmene amadzikondela yekha komanso mkazi azilemekeza kwambili mwamuna wake.”—Aefeso 5:33.
Baibo imakamba kuti
-
Anthu okwatilana ayenela kukhala okhulupilika kwa wina ndi mnzake.—Mateyo 19:4-6.
-
Ana amene amalemekeza ndi kumvela makolo ao zinthu zimawayendela bwino.—Aefeso 6:1-3.
Kuti mudziwe zambili, pitani pa jw.org.

