NSANJA YA MLONDA August 2013 | Kodi Zamalisece—Zilibe Vuto?

NKHANI YA PACIKUTO

Kodi Zamalisece Zilibe Vuto??

What effect does viewing pornography have on individuals and families?

BAIBO IMASINTHA ANTHU

“N’nayamba Kuganizila Kwambili za Moyo Wanga”

Ŵelengani nkhaniyi kuti mudziŵe mmene Baibo inathandizila munthu wina kusiya makhalidwe oipa komanso maganizo ake kuti ayambe kusangalatsa Mulungu.

Kuyankha Mafunso a M’baibo

N’cifukwa ciani mapemphelo ena sasangalatsa Mulungu? Kodi tiyenela kucita ciani kuti Mulungu amve mapemphelo athu?

TENGELANI CIKHULUPILILO CAWO

Anam’sunga “Pomupulumutsa Pamodzi ndi Anthu Ena 7”

How did Noah and his family survive the darkest hour humanity had ever known?

Madanga Ena Opezeka pa Intaneti

Kodi a Mboni za Yehova Amacita Nao Bwanji Anthu Amene Kale Anali m’Cipembedzo Cao?

A Mboni za Yehova amayesetsa kucitila aliyense zinthu mwacikondi ndi mwaulemu, kuphatikizapo anthu amene acotsedwa mumpingo.