Cinyanja
Nyuzi
https://assetsnffrgf-a.akamaihd.net/assets/ct/d71826a198/images/syn_placeholder_sqr.png

Nyuzi

 

2022-06-08

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Ciunikilo Na. 4 ca Bungwe Lolamulila mu 2022

Wa m’Bungwe Lolamulila akutilimbikitsa kupilila mayeso mokhulupilika komanso mwacimwemwe potengela citsanzo ca abale athu a kum’mawa kwa Europe.

2022-06-08

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Ciunikilo Na. 3 ca Bungwe Lolamulila mu 2022

Wa m’Bungwe lolamulila akufotokoza mfundo zimene zingatithandize kucepetsako nkhawa zimene tingakhale nazo tikaganizila za nkhondo imene ikucitika kum’mawa kwa Europe.

2022-03-09

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Ciunikilo Na. 2 ca Bungwe Lolamulila mu 2022

M’bale wa m’Bungwe Lolamulila akufotokoza mmene abale na alongo athu akhalilabe okhulupilika pamene akukumana na mayeso.

2021-02-08

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

2020—Ciunikilo Na. 9 ca Bungwe Lolamulila

M’bale wa m’Bungwe Lolamulila afotokoza kufunika kopitilizabe kukhala chelu na mmene tingadzitetezele ife tokha na anthu ena ku matenda a COVID-19.

2021-02-08

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

2020—Ciunikilo Na. 8 ca Bungwe Lolamulila

M’bale wa m’Bungwe Lolamulila afotokoza mmene maulosi a m’Baibo angatithandizile kupilila pa nthawi ya mliliwu.

2021-02-08

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

2020—Ciunikilo Na. 7 ca Bungwe Lolamulila

M’bale wa m’Bungwe Lolamulila afotokoza zimene zingathandize acicepele kupilila mavuto obwela cifukwa ca mliliwu.

2021-02-08

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Ciunikilo Na. 6 ca Bungwe Lolamulila mu 2020

Wa m’Bungwe Lolamulila afotokoza mmene cakudya cauzimu capitilizila kupelekedwa mosasamala kanthu za mlili.

2023-05-06

RUSSIA

Mlandu wa Mboni za Yehova Uloŵanso mu Khoti ku Taganrog—Kodi Cilungamo Cidzacitika Liti?

Kodi Mboni 16 zamtendele ku Russia zidzamangidwa cifukwa ca cikhulupililo cawo?