Nyuzi
NKHANI ZATSOPANO
Ciunikilo Na. 2 ca Bungwe Lolamulila mu 2026
M’ciunikilo cino, tidzafotokoza kamvedwe katsopano kokhudza mmene wodwala angaseŵenzetsele magazi ake pa nkhani zokhudza cithandizo ca cipatala.
NKHANI ZATSOPANO
Ciunikilo Na. 2 ca Bungwe Lolamulila mu 2026
M’ciunikilo cino, tidzafotokoza kamvedwe katsopano kokhudza mmene wodwala angaseŵenzetsele magazi ake pa nkhani zokhudza cithandizo ca cipatala.
Ciunikilo Na. 1 ca Bungwe Lolamulila mu 2026
M’ciunikilo cino, tikambilana malangizo atsopano a motsogozela maphunzilo a Baibo mogwila mtima pogwilitsila nchito buku lakuti, Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!
Ciunikilo Na. 8 ca Bungwe Lolamulila mu 2025
M’ciunikilo cino, tione mmene mavidiyo a sewelo yakuti, Mbili ya Umoyo wa Yesu akukhudzila abale ndi alongo athu.
Ciunikilo Na. 7 ca Bungwe Lolamulila mu 2025
M’ciunikilo cino, tione zocitika zosangalatsa za mu Lipoti la Caka ca Utumiki ca 2025. Tionanso mmene Yehova akudalitsila nchito yathu yolalikila pa dziko lonse.
Ciunikilo Na. 6 ca Bungwe Lolamulila mu 2025
M’ciunikilo cino tikambilane zokhudza lemba la caka ca 2026 komanso nyimbo yatsopano.
Ciunikilo Na. 5 ca Bungwe Lolamulila mu 2025
M’ciunikilo cino, tikambilana mfundo zimene zingatithandize kupanga zisankho zanzelu pa nkhani yoonjezela maphunzilo a kuthupi.
Ciunikilo Na. 4 ca Bungwe Lolamulila mu 2025
M’ciunikilo cino, tikambilana mfundo za m’Baibo zimene zingatithandize kupanga zisankho zanzelu pa nkhani ya zizindikilo ndi miyambo.
Ciunikilo Na. 3 ca Bungwe Lolamulila mu 2025
M’ciunikilo cino, tiona zimene tingacite kuti tikhale ndi zocita zambili zauzimu m’miyezi ingapo ikubwelayi.
Ciunikilo Na. 2 ca Bungwe Lolamulira mu 2025
Mu ciunikilo cino, tikambilana zimene tacita posacedwa kuti tithandize anthu kudziwa kuwerenga ndi kulemba. Tikambilanenso za mtendere umene timapeza cifukwa ca nsembe ya dipo la Yesu. Cina, tilengeze za kutulutsidwa kwa nyimbo yatsopano imene idzaimbidwa pa msonkhano wacigawo wa 2025.
Ciunikilo Na. 1 ca Bungwe Lolamulila mu 2025
Mu ciunikilo cino, tiona mmene tingagwilitsile nchito mbali yakuti “Mfundo za m’Baibo Zimene Timafunitsitsa Kuphunzitsa Anthu” yopezeka ku zakumapeto A m’bulosha yakuti Kondani Anthu Kuti Mupange Ophunzila. Kuphunzila mfundo za coonadi zimenezi, kudzatithandiza kukhala ndi makambilano osangalatsa mu ulaliki.
Ciunikilo Na. 8 ca Bungwe Lolamulila mu 2024
Mu Ciunikilo cino, tiona kufunika kowaona moyenela abale ndi alongo amene amaonekela m’mavidiyo athu.
Ciunikilo Na 7 ca Bungwe Lolamulila mu 2024.
Mu Ciunikilo cino, tiimve mmene zinthu zilili kwa abale ndi alongo athu m’maiko osiyanasiyana. Kuonjezela apo, tikhalenso ndi mwayi wokambilana ndi abale awili, m’bale Jody Jedele ndi m’bale Jacob Rumph amene ndi mamembala atsopano a Bungwe lolamulila.
Ciunikilo Na. 6 ca Bungwe Lolamulila mu 2024
M’ciunikilo cino, tione zimene tingacite kuti tipitilize kuyambitsa maphunzilo a Baibulo.
Ciunikilo Na. 5 ca Bungwe Lolamulila mu 2024
Mu ciunikilo cino, tiphunzile zimene zingatithandize kuti tiziika maganizo athu pa Ufumu wa Mulungu omwe ndiwo yankho lokha la mavuto amene timakumana nawo.
Ciunikilo Na. 4 ca Bungwe Lolamulila mu 2024
Mu ciunikilo cino, tiona mmene abale na alongo amene ali mundende cifukwa ca cikhulupililo cawo ‘akugonjetsela coipa mwa kucita cabwino.’—Aroma 12:21.

