Pulogiramu ya Msonkhano wa Dera wa 2025-2026 Wokhala ndi Woimira Nthambi
‘Mverani Zimene Mzimu Ukunena ku Mipingo’
Pulogiramu ya cigawo ca m’maŵa komanso ca madzulo ca msonkhano wa dera wokhala ndi woimira nthambi.
Pezani Mayankho pa Mafunso Aya
Mafunsowa adzayankhidwa pa msonkhano uno.

