NSANJA YA MLONDA

Mau Oyamba

Cinyanja
Mau Oyamba
/assets/ct/28ada02fb0/images/syn_placeholder_sqr.png

Mau Oyamba

Mau Oyamba

MUGANIZA BWANJI?

Kodi Baibo ni yothandiza masiku ano kapena si yothandiza? Baibo imayankha yokha kuti: “Malemba onse anauzilidwa ndi Mulungu, ndipo ndi opindulitsa.”2 Timoteyo 3:16, 17.

Nsanja ya Mlonda iyi ifotokoza ena mwa malangizo othandiza opezeka m’Baibo, ndipo ikambanso zimene mungacite kuti mupindule na zimene mumaŵelenga m’Baibo.