NSANJA YA MLONDA September 2012

NKHANI YA PACIKUTO

Mulungu Amafuna Kuti Akazi Azilemekezedwa

Kodi tiphunzilanji pa khalidwe la Yesu na maganizo ake kwa akazi?

PHUNZILANI M’MAWU A MULUNGU

Kodi pa Tsiku la Ciweluzo Padzacitika Zotani?

Anthu amakhulupilila zosiyana-siyana zokhudza tsiku la ciweluzo. Kodi pali cofunika kuopa? Kodi lidzakwanilitsa ciani?

OŴELENGA AKUFUNSA

Kodi Akazi a Mboni za Yehova Amaphunzitsa Mawu a Mulungu?

Conco kodi amatsatila Mfundo iti ya m’Baibo? Kodi amacita utumiki wotani?

Mungakondenso Izi

ZOKHUDZA IFE MBONI

Pemphani kuti wa Mboni adzakucezeleni

Kambilanani nkhani ya m’Baibo na Mboni za Yehova, kapena laŵani maphunzilo a Baibo amene timapeleka.