NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA August 2015

Magazini ino ili ndi nkhani zophunzila kuyambila mlungu wa September 28 mpaka October 25, 2015.

MBILI YANGA

“Zilumba Zambili Zisangalale”

Ŵelengani mbili ya m’bale Geoffrey Jackson, amene akutumikila m’Bungwe Lolamulila

Muzisinkhasinkha za Cikondi Cosatha ca Yehova

Kodi mungatsimikize bwanji kuti Yehova ali ndi inu panthawi ya mavuto?

Yembekezelanibe!

Tili ndi zifukwa ziŵili zazikulu zimene ziyenela kutipangitsa kukhala maso pamene mapeto akuyandikila.

Konzekelani Kudzakhala ndi Moyo m’Dziko Latsopano

Zocita za anthu a Mulungu zimafanana ndi za anthu amene akufuna kusamukila m’dziko lina.

Samalani Ndi Anthu Ogwilizana Nao Masiku Ano Otsiliza

Anzanu si anthu okha amene mumaceza nao.

Kodi Tiphunzilapo Ciani pa Zimene Jowana Anacita?

N’ciani cimene anasintha pa umoyo wake kuti akhale wotsatila wa Yesu?

ZA M'NKHOKWE YATHU

“Yehova Wakubweletsani Kuno ku France kuti Muphunzile Coonadi”

Pangano limene dziko la France ndi la Poland linacita mu 1919, lolola anthu a ku Poland kusamukila ku France linakhala ndi zotsatilapo zabwino.