Kodi n’zotheka kukhala ndi moyo kwamuyaya?
“Olungama adzalandila dziko lapansi, ndipo adzakhala mmenemo mpaka kalekale.”—Salimo 37:29.
Baibo imakamba kuti m’tsogolo
-
Matenda onse adzatha.—Yesaya 33:24; 35:5, 6.
-
Zacilengedwe zimene zaonongedwa zidzakonzedwanso ndipo dziko lidzakhala paradaiso.—Yesaya 35:1, 2; Chivumbulutso 11:18.
Kuti mudziwe zambili, pitani pa jw.org.

