Kodi imfa ndi mapeto a zonse?

Kodi Imfa ndi Mapeto a Zonse?

Cinyanja
Kodi Imfa ndi Mapeto a Zonse?
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102024315/afrn/art/1102024315_afrn_sqr_xl.jpg
T-dth masa. 1-2

Kodi imfa ndi mapeto a zonse?

Kodi imfa ndi mapeto a zonse?

“Nthawi ikubwela pamene onse ali m’manda acikumbutso adzamva mau [a Yesu] ndipo adzatuluka.”​Yohane 5:​28, 29.

Baibo imatitsimikizila kuti

  • Mulungu adzaukitsa okondedwa athu amene anamwalila.​Machitidwe 24:15.

  • Iye amafunitsitsa kuti adzawaukitse.​Yobu 14:​13-15.

Kuti mudziwe zambili, pitani pa jw.org.