Mabulosha ndi Tumabuku

Mu mabulosha athu ndi tumabuku muli nkhani zosiyana-siyana za m’Baibo. Mumapezeka mfundo zambili kuposa zimene zimapezeka m’mathilakiti kapena mu nkhani zina. Koma mfundo zake sizikhala zambili poyelekeza ndi zimene zimapezeka m’mabuku.

ONANI