Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Sitili Tekha

Sitili Tekha

Daunilodi:

  1. 1. Anthu anikana.

    Ine navutika.

    Nkhawa zaculukitsa.

    Moyo wanilemetsadi.

    Nilibe anzanga

    Anganithandize.

    Onitonthoza ndani?

    Ndani adzanithandiza?

    (KOLASI)

    Munalipo, mukalipo

    Mudzakhalapo Yehova.

    Mumadziŵa, mumaona

    Mumamvela Nikapempha.

    Olo nivutike, sinili nekha.

  2. 2. Olo nivutike cifukwa ca imwe,

    Ena anganisiye, koma simunganisiye.

    Ndimwe M’lungu wanga.

    Mulidi pafupi, nimadalila imwe.

    Simunganitailile.

    (KOLASI)

    Munalipo, mukalipo

    Mudzakhalapo Yehova.

    Mumadziŵa, mumaona

    Mumamvela Nikapempha.

    Olo nivutike, sinili nekha.

    Munalipo, mukalipo

    Mudzakhalapo Yehova.

    Mumadziŵa, mumaona

    Mumamvela Nikapempha.

    Olo nivutike, sinili nekha.