Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Mtendele Wosatha Pamapeto Pake! (2022 Nyimbo ya Pamsonkhano Wacigawo)

Mtendele Wosatha Pamapeto Pake! (2022 Nyimbo ya Pamsonkhano Wacigawo)

Daunilodi:

  1. 1. M’dziko lamavuto

    Anthu a M’lungu

    akukhala pamtendele.

    Ndipo tidziŵa kuti mavutowa

    adzathadi posacedwa.

    (KOLASI)

    Pamapeto pake tidzauona

    mtendele wosatha.

    Pa dziko lapansi na kumwambako,

    konse kudzakhala mtendele.

  2. 2. M’dziko latsopano anthu onse

    adzakhaladi amodzi.

    Ulamulilo tidzauonewo

    udzakhala wacikondi.

    (KOLASI)

    Pamapeto pake tidzauona

    mtendele wosatha.

    Pa dziko lapansi na kumwambako,

    konse kudzakhala mtendele.

    (KOLASI)

    Pamapeto pake tidzauona

    mtendele wosatha.

    Pa dziko lapansi na kumwambako,

    konse kudzakhala.

    (KOLASI)

    Pamapeto pake tidzauona

    mtendele wosatha.

    Pa dziko lapansi na kumwambako,

    konse kudzakhala

    mtendele,

    mtendele!