Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Pezani Mayankho pa Mafunso Aya

Pezani Mayankho pa Mafunso Aya
  1. 1. Ni zinthu zitatu ziti zocokela kwa Yehova zimene zimatipatsa cimwemwe? (Sal. 32:1-10)

  2. 2. Kodi tingakhale bwanji acimwemwe pali pano? (Sal. 5:11, 12; 91:14)

  3. 3. Kodi tingakhale bwanji acimwemwe mu ulaliki olo kuti tikukumana na zovuta? (Mac. 13:50-52; Aroma 5:3-5)

  4. 4. Kodi tingapewe bwanji ‘kulemedwa’ na kutaya cimwemwe cathu? (Luka 21:34)

  5. 5. Kodi Yehova amatipangitsa bwanji kukhala acimwemwe?(Sal. 92:4, 5)

  6. 6. N’ciani cidzatithandiza kuika Yehova patsogolo pathu nthawi zonse? (Aroma 1:20; Deut. 6:6-9; Afil. 4:6; Sal. 16:3)