Pulogilamu ya Msonkhano Wadela ya 2020-2021—Na Woimila Nthambi

Onani pulogilamu ya msonkhano wadela yokhala na nkhani zokambidwa na woimila nthambi. Mutu wa msonkhanowu ukuti, Kondwelani mwa Yehova

Kondwelani Mwa Yehova

Pulogilamu ya msonkhano wadela na woimila nthambi, yoonetsa cigawo ca m’maŵa komanso ca masana.

Pezani Mayankho pa Mafunso Aya

Mafunso ano aziyankhidwa mkati mwa msonkhano.