Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Sipanawonongeke Ciliconse

Sipanawonongeke Ciliconse

Yesu atadyetsa mozizwitsa amuna 5,000 kuphatikizapo azimayi na ŵana, anauza ophunzila ake kuti: “Sonkhanitsani zotsala zonse, kuti pasawonongeke ciliconse.” (Yoh. 6:12) Yesu anaonetsa kuyamikila pa zimene Yehova anawapatsa mwa kusawononga ciliconse.

Masiku ano, Bungwe Lolamulila limayesetsa kutengela citsanzo ca Yesu mwa kuseŵenzetsa bwino zopeleka zaufulu. Mwacitsanzo, pomanga likulu lathu ku Warwick, mu mzinda wa New York, abale anasankha pulani ya kamangidwe yosawonongetsa kwambili zopeleka zaufulu.

TINGAPEWE BWANJI KUKHALA WOWONONGA . . .