UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO September 2018
Makambilano Acitsanzo
Makambilano otsatizana-tsatizana a mmene Mulungu amaonela anthu.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Yesu Acita Cozizwitsa Cake Coyamba
Cozizwitsa coyamba ca Yesu citithandiza kudziŵa bwino umunthu wake.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Yesu Alalikila Mayi Wacisamariya
Kuti Yesu acite ulaliki wa mwayi, anayambitsa makambilano mwa kuseŵenzetsa cinthu codziŵika kwa mayiyo.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kuyambitsa Makambilano Otsogolela ku Ulaliki
Kodi tinganole bwanji luso lathu loyambitsa makambilano na ŵanthu amene sitiwadziŵa?
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Tsatilani Yesu na Colinga Cabwino
Ophunzila ena anakhumudwa ndipo analeka kutsatila Yesu cifukwa anali na zolinga zadyela.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Sipanawonongeke Ciliconse
Monga Yesu, tingaonetse kuyamikila pa zimene Yehova watipatsa mwa kusakhala wowononga.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Yesu Analemekeza Atate Wake
Cacikulu kwa Yesu cinali kukwanilitsa nchito imene Yehova anam’patsa.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Onetsani Khalidwe la Kudzicepetsa Monga Khristu
Tingatengele bwanji citsanzo ca Yesu pamene tapatsidwa udindo mu mpingo?