Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 20-22

“Taonani! Zinthu Zonse Zimene Ndikupanga N’zatsopano”

“Taonani! Zinthu Zonse Zimene Ndikupanga N’zatsopano”

21:1-5

Yehova walonjeza kuti adzapanga zinthu zonse kukhala zatsopano.

  • “Kumwamba kwatsopano”: Boma latsopano limene lidzabweletsa cilungamo na kukonza zinthu zonse pa padziko lapansi

  • “Dziko lapansi latsopano”: Anthu amene amagonjela ulamulilo wa Mulungu na kutsatila miyezo yake yolungama

  • “Zinthu zonse . . . n’zatsopano”: Mavuto onse na nkhaŵa zidzalowedwa m’malo na maganizo osangalatsa tsiku lilonse