Alongo ku Switzerland akutambitsa vidiyo ya mu Thuboksi yathu

UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO December 2019

Makambilano Acitsanzo

Makambilano otsatizana-tsatizana okamba za Baibo na umoyo wacimwemwe.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Khamu Lalikulu Losaŵelengeka Likudalitsidwa na Yehova

Mungacite ciani kuti mukhale mmodzi wa khamu lalikulu na kulandilako madalitso?

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

‘Mboni Ziŵili’ Zinaphedwa, Kenako Zinakhalanso na Moyo

Kodi masomphenya a mboni ziŵili amene mtumwi Yohane anaona atanthauzanji?

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Dzikolo ‘Linameza Mtsinje’

Kodi Yehova amawathandiza bwanji anthu amene amangidwa cifukwa ca cikhulupililo cawo?

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Musamaope Zilombo Zoopsa

Kodi tingapewe bwanji kutengela zocita za cilombo cochulidwa pa Chivumbulutso 13?

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Nkhondo ya Mulungu Idzathetsa Nkhondo Zonse

N’cifukwa ciani Mulungu adzamenya nkhondo? Nanga tingacite ciani kuti tikapulumuke?

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Taonani! Zinthu Zonse Zimene Ndikupanga N’zatsopano”

Kodi Mulungu adzapanga bwanji zinthu zonse kukhala zatsopano? Nanga kodi zimenezi zidzatanthauzanji?

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Khalani Okonzeka Kusintha Ulaliki

Tingacite ciani kuti tizikhala okonzeka kusintha ulaliki?