Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

April 29–May 5

2 AKORINTO 1-3

April 29–May 5
  • Nyimbo 44 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Yehova ni ‘Mulungu Amene Amatitonthoza M’njila Iliyonse’”: (10 min.)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • 2 Akor. 1:22—Kodi “cikole” komanso “cidindo” cimene Mkhristu aliyense wodzozedwa amalandila kucokela kwa Mulungu ciani? (w16.04 32)

    • 2 Akor. 2:14-16—Kodi mtumwi Paulo ayenela kuti anatanthauza ciani pamene anakamba za ‘kuguba pa cionetselo conyadilila kupambana’? (w10 8/1 23)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 2 Akor. 3:1-18 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU