Phunzilo 3: Muzipemphela Nthawi Zonse
Imbani nyimbo limodzi ndi Sofiya yokhudza kupemphela kwa Yehova nthawi zonse ndi kulikonse.
Mungakondenso Izi
ZIMENE BAIBO IMAPHUNZITSA
Zocita za Ana
Seŵenzetsani zocita zosangalatsazi, zozikika pa Baibo, pophunzitsa ana makhalidwe auzimu.