Onani zimene zilipo

Kukaona Malo pa Beteli

Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.

Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.

New Caledonia

236, rue Georges Lèques

Normandie

98800 NOUMEA

NEW CALEDONIA

+687 43-75-00

Kuona Malo

Pa Mande mpaka pa Cisanu

8:00hrs mpaka 11:00hrs ndi 13:00hrs mpaka 16:00hrs.

Nthawi yoona malo: Mphindi 45

Zimene Timacita

Timayang’anila nchito ya Mboni za Yehova m’dzikoli, ku Vanuatu ndi ku zilumba za Wallis ndi Futuna. Timamasulila mabuku ofotokoza Baibulo m’Ciwalisi, Cilifu, Cibisilama ndiponso m’zinenelo zina zisanu za m’dzikoli.

Tengani kapepala koonetsa malo.