Khala Bwenzi la Yehova—Nyimbo Zopekedwa Koyamba

Aka ni kagulu ka nyimbo zimene zimafika ana pamtima.

Uzilemekeza Acikulile

Ungaonetse bwanji kuti umalemekeza acikulile amene atumikila Yehova kwa zaka zambili?

Uziyamikila

Ungaonetse bwanji kuti umayamikila anthu amene amakucitila zabwino?