NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA October 2015

Maganiziyi ili ndi nkhani zophunzila mlungu wa November 30 mpaka December 27, 2015.

Kodi Mumaona Dzanja la Mulungu pa Umoyo Wanu?

Kodi Baibulo limatanthauza ciani likanena kuti “dzanja” la Mulungu?

“Tionjezeleni Cikhulupililo”

Kodi tikhoza kukhala ndi cikhulupililo mwa mphamvu zathu zokha?

Tumikilani Yehova Popanda Cosokoneza

Pafupifupi zaka 60 zapitazo, Nsanja ya Olonda inafotokoza zinthu zina zake zimene zinadzakhala zolondola pambuyo pake.

Pitilizani Kusinkhasinkha Zinthu za Kuuzimu

Kodi n’zotheka kukhalabe wathanzi mwakuuzimu ngakhale kuti mulibe Baibulo?

‘Abale Okhala Ngati Amenewa Muziwalemekeza Kwambili’

Ndani amene akuthandizila makomiti a Bungwe Lolamulila? Kodi nchito yao ndi yotani?

MBILI YANGA

Kwa Ine Kuyandikila Mulungu ndi Cinthu Cabwino

Pamene Sarah Maiga anakwanitsa zaka 9, iye analeka kukula kuthupi, koma osati kuuzimu.

“Munthu Amene Sadziŵa Zinthu Amakhulupilila Mau Alionse”

Kodi tingawadziŵe bwanji anthu abodza, akuba, ndiponso nkhani zina zabodza zimene wina watitumila?