NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA January 2015

M’magazini ino muli nkhani zophunzila mlungu wa March 2, 2015, mpaka April 5, 2015.

Anadzipeleka Mofunitsitsa Ku New York

N’cifukwa ciani banja lina linasamuka m’nyumba yao yokongola ndi kupita m’kanyumba kakang’ono?

Yamikani Yehova Ndipo Mudzadalitsidwa

Kodi kuyamikila kungatithandize bwanji kupilila mavuto?

Cifukwa Cake Timacita Mgonelo wa Ambuye

Kodi mungadziŵe bwanji kuti Mulungu wakupatsani ciyembekezo cakumwamba kapena ca padziko lapansi?

Khalani ndi Banja Lolimba ndi Lacimwemwe

Gwilitsilani nchito njila zisanu kuti banja likhale lolimba ndi lacimwemwe.

Lolani Yehova Kulimbitsa ndi Kuteteza Ukwati Wanu

N’ciani cimene muyenela kucita kuti mupewe kucita cigololo ndiponso zotsatilapo zake zoipa?

Kodi N’zotheka Kukhala m’Cikondi Ceniceni?

Anthu amene ali pa banja ndiponso amene sali pa banja angaphunzile zinthu zothandiza m’nkhani ya cikondi imene ili m’Nyimbo ya Solomo.