NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA October 2018

Magazini ino ili na nkhani zophunzila wiki ya December 3-30, 2018.

1918—Zimene Zinacitika Zaka 100 Zapitazo

Nkhondo Yoyamba ya Dziko Lonse inali ikali mkati ku Europe. Koma zimene zinacitika kuciyambi kwa cakaco, zinaonetsa kuti zinthu zidzayenda bwino kwa Ophunzila Baibo, komanso kwa anthu pa dziko lonse.

Tizikamba Zoona

N’cifukwa ciani anthu amanama, nanga pamakhala zotulukapo zanji? Tingaonetse bwanji kuti timakamba zoona kwa wina na mnzake

Kuphunzitsa Coonadi

Cifukwa cakuti tatsala na nthawi yocepa yocitila umboni, colinga cathu cacikulu ciyenela kukhala kuyambitsa maphunzilo a Baibo na kuphunzitsa anthu coonadi. Kodi zida za mu Thuboksi yathu zingatithandize bwanji?

MBILI YANGA

Yehova Anan’dalitsa Kwambili Cifukwa ca Zimene N’nasankha

Pamene anali wacinyamata, Charles Molohan anawonjezela utumiki wake mwa kufunsila utumiki wa pa Beteli. Kucokela nthawi imeneyo, Yehova wakhala akum’dalitsa.

Tizidalila Mtsogoleli Wathu—Khristu

Pamene gulu la Mulungu likupita patsogolo mofulumila kwambili, kodi tili na zifukwa ziti zotipangitsa kudalila utsogoleli wa Khristu masiku ano?

Khalanibe na Mtendele wa mu Mtima Olo Pamene Zinthu Zasintha

Zinthu zikasintha mosayembekezeleka mu umoyo wathu, tingakhale na nkhawa yaikulu. Kodi “mtendele wa Mulungu” ungatithandize bwanji?

Kodi Mudziŵa?

Sitefano anakhala Mkhristu woyamba kufela cikhulupililo cake. N’ciani cinamuthandiza kukhalabe wodekha pamene anali kuzunzidwa?