NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA July 2016

Magazini ino ili na nkhani zophunzila kuyambila mlungu wa August 29 mpaka September 25, 2016.

Anadzipeleka na Mtima Wonse—Ku Ghana

Ngakhale kuti kutumikila kumene kufunika ofalitsa Ufumu ambili kuli na mavuto ake, madalitso ni ambili.

Muzifuna-funa Ufumu, Osati Zinthu Zakuthupi

Yesu anafotokoza cifukwa cake sitiyenela kulakalaka zinthu zakuthupi.

N’cifukwa Ciani Tiyenela ‘Kukhalabe Maso’?

Pali zinthu zitatu zimene zingatilepheletse kukhala maso ngati sitinasamale.

“Usacite Mantha. Ndikuthandiza”

Yehova amaonetsa kuti ni bwenzi lokhulupilika tikakumana ndi mavuto.

Tiziyamikila Kukoma Mtima Kwakukulu Kumene Tinalandila

Ni njila yaikulu iti imene Mulungu anaonetsela kukoma mtima kwake kwakululu kwa anthu?

Lalikilani Uthenga Wabwino Wokamba za Kukoma Mtima

Kodi “uthenga wabwino wa Ufumu” umaonetsa bwanji kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu?

Mafunso Ocokela kwa Aŵelengi

Ezekieli caputala 37 imafotokoza ndodo ziŵili zimene zinakhala ndodo imodzi. Kodi izi zitanthauza ciani?