NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA August 2016

Magaziniyi ili na nkhani zophunzila mlungu wa September 26 mpaka October 23, 2016.

MBILI YANGA

Napeza Cimwemwe Cifukwa Copatsa

Wacicepele wa ku England anayamba kukhala umoyo umene wam’patsa cimwemwe, anakhala m’mishonale ku Puerto Rico.

Cikwati—Ciyambi na Cifuno Cake

Kodi cikwati cinacokeladi kwa Mulungu?

Fufuzani Cinthu Camtengo Wapatali Kuposa Golide

Dziŵani njila zitatu za mmene ophunzila Baibulo acangu amafananila ndi ofufuza golide.

Kodi Mumaona Kufunika Kopita Patsogolo Kuuzimu?

Dziŵani zimene mungacite kuti mukwanitse.

Kodi Mumaona Kufunika Kophunzitsa Ena?

Ni zolinga zofunika ziti zimene mungawathandize kukwanilitsa?

Mafunso Ocokela Kwa Aŵelengi

N’cifukwa ciani adani a Yesu anakhumudwa na nkhani yosamba m’manja?

ZA M'NKHOKWE YATHU

“Nikolola Zipatso ndi Kutamanda Yehova”

Ngakhale kuti Ophunzila Baibulo sanali kumvetsetsa nkhani ya kusatengako mbali m’nkhondo pa nkhondo ya padziko lonse, kuona mtima kwawo kunali ndi zotulukapo zabwino.