NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA May 2019

Magazini ino ili na nkhani zophunzila wiki ya July 1-August 4, 2019.

Cikondi na Cilungamo Mumpingo Wacikhristu

Kodi cilamulo cimeneci ciphatikizapo ciani? Nanga cimalimbikitsa bwanji cilungamo?

Cikondi na Cilungamo M’dziko Loipali

Kodi makolo angateteze bwanji ana awo kwa anthu ocitila ana zolaula? Nanga kodi akulu angateteze bwanji mpingo kwa anthu ocitila ana zolaula?

Kulimbikitsa Amene Anacitilidwapo Zolaula

Kodi anthu amene anacitilidwapo zolaula angalimbikitse bwanji na Mawu a Mulungu, akulu, komanso alongo acikulile mwauzimu?

Musasoceletsedwe na “Nzelu za M’dzikoli”

N’cifukwa ciani Yehova yekha ndiye Gwelo lodalilika la malangizo? Kodi Baibo imatithandiza bwanji kudziona moyenelela?

Khalani na Cizoloŵezi Cabwino Coŵelenga

Kodi tingasankhe bwanji zinthu zofunika kuika patsogolo muumoyo kuti tizipindula kwambili na phunzilo laumwini?