GALAMUKA! Na. 3 2019 | Kodi Baibo Ingakuthandizeni Kukhala na Umoyo Wabwino?

Kwa zaka zambili, Baibo yathandiza anthu kukhala na umoyo wabwino. Mungapindule na malangizo ake othandiza mu umoyo wa tsiku na tsiku.

Buku Lakale-kale, Koma Lothandiza Masiku Ano

Onani zimene ena amakamba ponena za kuŵelenga na kuseŵenzetsa malangizo a m’Baibo mu umoyo wawo.

Thanzi Labwino

Mfundo za m’Baibo zimatilimbikitsa kucita zonse zotheka kuti tisamalile thanzi lathu.

Kudziŵa Kulamulila Mtima Wathu

Timapindula tikamayesetsa kulamulila mtima wathu.

Umoyo wa Banja Komanso Mabwenzi

Kuti ubwenzi ukhale wolimba, tifunika kuika maganizo athu pa kukhala wopatsa m’malo mwa kulandila.

Moseŵenzetsela Ndalama

Kodi mfundo za m’Baibo zingakuthandizeni bwanji kucepetsa mavuto a za ndalama?

Umoyo Wauzimu

Miyezo ya Mulungu komanso mfundo za m’Baibo zingakuthandizeni kukhala na umoyo wauzimu wabwino. Onani mmene izi zingakuthandizileni.

Buku Lothandiza Kwambili m’Mbili Yonse ya Anthu

Ziŵelengelo zionetsa kuti, Baibo ni buku imene yamasulilidwa na kufalitsidwa kuposa buku lina lililonse.

Za m’Kope Ino ya Galamuka!: Kodi Baibo Ingakuthandizeni Kukhala na Umoyo Wabwino?

Baibo ili na malangizo othandiza mu umoyo wathu wa tsiku na tsiku.