Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

NSANJA YA MLONDA Na. 2 2021 | Dziko Labwino Lili Pafupi

Kodi zinthu zimene zikucitika padzikoli n’cizindikilo cakuti dziko lili pafupi kutha? Ngati n’conco, kodi pali zimene tingacite kuti tikapulumuke mapeto a dzikoli? Nanga n’ciani cidzacitika dziko likadzatha? Nkhani za m’magazini ino, zidzapeleka mayankho a m’Baibo okhazika mtima pansi pa mafunso amenewa.

 

Tifunikila Dziko Labwino!

Zinthu zimene zikucitika padzikoli zionetsa kuti tifunika dziko labwino.

Kodi Dzikoli Lidzatha?

Baibo imakamba kuti dzikoli lidzatha, koma imakambanso kuti pa dziko lapansi padzakhalabe anthu nthawi zonse.

Kodi Mapeto Adzafika Liti? Zimene Yesu Anakamba

Kodi mumaziona zinthu zimene Yesu anakambilatu kuti zidzacitika?

Zimene Mungacite Kuti Mukakhalemo m’Dziko Latsopano

Kodi kukhala pa ubwenzi na Mulungu n’kofunika bwanji kuti munthu akapulumuke?

Dziko Latsopano la Paradaiso Limene Lili Pafupi!

Kodi zinthu zidzakhala bwanji padziko lapansi Mulungu akadzakwanilitsa malonjezo ake?

Kodi Mapeto a Dzikoli Ali Pafupi?

Mungadabwe na yankho la m’Baibo pa funso limeneli.