Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

GALAMUKA! Na. 3 2020 | Kodi Kuli Mankhwala Othetsela Tsankho?

Ambili a ife timaliona khalidwe la tsankho mwa anthu ena. Koma zingakhale zovuta kuzindikila kuti nafenso tili nalo khalidweli.

Onani mfundo zina zimene zingatithandize kulimbana na khalidwe la tsankho.

 

Tsankho—Kodi Na Imwe Muli Nalo?

Ni zinthu ziti zimene zingaonetse kuti tili na tsankho?

Dziŵani Zoona Zeni-zeni

Mabodza amene tingamvele angatipangitse kuona ena molakwika. Onani mmene citsanzo ca zocitika zeni-zeni ca munthu amene kale anali msilikali cikuonetsela bwino zimenezi.

Onetsani Cifundo

Kodi kusoŵa cifundo kungakhale cizindikilo ca ciani?

Onani Zimene Ena Amacita Bwino

Kudzikuza kumayambitsa tsankho. Kodi mankhwala ake n’ciani?

Pezani Mabwenzi a Mitundu Yosiyana-siyana

Onani mapindu okhala na mabwenzi osiyana na imwe.

Onetsani Cikondi

Kuonetsa cikondi kumathetsa tsankho. Ganizilani zimene mungacite.

Mankhwala Amene Adzathetselatu Tsankho

Ni zinthu zinayi ziti zimene Ufumu wa Mulungu udzacita kuti uthetse tsankho?

Anagonjetsa Tsankho

Tambani mavidiyo atatu kuti muone mmene anthu ena anathetsela tsankho mumtima mwawo.