Pulogilamu ya Msonkhano wa Cigawo wa 2024 wakuti “Lengezani Uthenga Wabwino!”

Tsiku Loyamba

Pulogilamu ya tsiku loyamba yazikika pa Luka 2:10​—“Uthenga wabwino wa cimwemwe cacikulu cimene anthu onse adzakhale naco.”

Tsiku Laciŵili

Pulogilamu ya tsiku laciŵili yazikika pa Salimo 96:2​—“Tsiku ndi tsiku muzilengeza uthenga wabwino wa cipulumutso cake.”

Tsiku Lacitatu

Pulogilamu ya pa tsiku lothela yazikika pa Mateyu 24:14​—“. . . kenako mapeto adzafika.”

Mawu kwa Osonkhana

Mawu othandiza opezeka pa msonkhano wa cigawo.

Mungakondenso Izi

ZOKHUDZA IFE MBONI

Kapezekemponi pa Msonkhano wa Cigawo wa 2024 wakuti​—Lengezani Uthenga Wabwino!

Tikuitanilani kuti mukapezeke ku msonkhano wa cigawo wa Mboni za Yehova wa masiku atatu.