Lipoti la Caka ca Utumiki ca 2020 la Mboni za Yehova Padziko Lonse

Onani mfundo zokhudza nchito yolalikila ya Mboni za Yehova padziko lonse kucokela mu September 2019 mpaka mu August 2020.

Ziŵelengelo Zonse za mu 2020

Lipoti limeneli la caka ca 2020 la Mboni za Yehova litionetsa khama komanso cuma zimene iwo anaseŵenzetsa pa nchito yolalikila padziko lonse.

Lipoti la 2020 la Maiko na Madela

Lipoti limeneli lili na ciŵelengelo ca Mboni, obatizika, opezeka pa Cikumbutso, komanso zina.

Mungakondenso Izi

MAFUNSO AMENE AMAFUNSIDWA KAŴILI-KAŴILI

N’cifukwa Ciani Mboni za Yehova Zimalalikila Kunyumba ndi Nyumba?

Normal;Onani zimene Yesu anauza ophunzila ake oyambilila kuti azicita.

MAVIDIYO OYAMBILAPO ULALIKI

Kodi Mboni za Yehova ni Anthu Otani?

Anthu ambili amafuna kudziŵa kuti Mboni za Yehova ni anthu otani. Fufuzani zokhudza iwo.

ZOKHUDZA IFE MBONI

Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji?

Zungulile dziko lonse, Mboni za Yehova zimadziŵika cifukwa ca pulogilamu yawo yophunzitsa Baibo kwaulele. Onani mmene imacitikila.