N’zotheka Banja Lanu Kukhala Lacimwemwe
Cikwati canu ndi banja lanu lingakhale lacimwemwe ngati mutsatila mfundo za m’Baibulo.
GAWO 1
Dalilani Mulungu Kuti Banja Lanu Likhale Lacimwemwe
Mafunso Aŵili Osavuta Amene Angathandize Banja Lanu Mukawagwilitsila Nchito.
GAWO 2
Khalani Wokhulupilika kwa Wina ndi Mnzake
Kodi kukhala wokhulupilika m’cikwati kumangotanthauza kupewa cigololo?
GAWO 3
Mmene Mungathetsele Mavuto
Kupeza njila yabwino yothetsela mavuto kungacititse kuti banja lanu likhale lolimba komanso lacimwemwe m’malo mokhala losalimba ndi lamavuto.
GAWO 4
Mmene Mungagwilitsile Nchito Ndalama
Kodi kukhala wokhulupilika ndi woona mtima kumathandiza bwanji?
GAWO 5
Mmene Mungakhalile Mwamtendele ndi Acibale Anu
Mungalemekeze makolo anu popanda kusokoneza cikwati canu.
GAWO 7
Mmene Mungaphunzitsile Mwana Wanu
Kulanga kumaphatikizapo zambili osati kungopeleka malamulo ndi cilango coŵaŵa.
GAWO 9
Lambilani Yehova Monga Banja
Mungacite ciani kuti muzisangalala kwambili ndi kulambila kwanu kwa pabanja?