Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

FUNSO 9

N’cifukwa ciani anthu amavutika?

N’cifukwa ciani anthu amavutika?

“Anthu othamanga kwambili sapambana pampikisano, amphamvu sapambana pankhondo, anzelu sapeza cakudya, omvetsa zinthu naonso sapeza cuma, ndipo ngakhale odziŵa zinthu sakondedwa, cifukwa nthawi yatsoka ndi zinthu zosayembekezeleka zimagwela onsewo.”

Mlaliki 9:11

“Ucimo unalowela m’dziko kudzela mwa munthu mmodzi, ndi imfa kudzela mwa ucimo, imfayo n’kufalikila kwa anthu onse cifukwa onse anacimwa . . .”

Aroma 5:12

“Conco, Mwana wa Mulungu anaonekela kuti aononge nchito za Mdyelekezi.”

1 Yohane 3:8

“Dziko lonse lili m’manja mwa woipayo.”

1 Yohane 5:19