Pulogilamu ya Msonkhano wa Dera wa 2025-2026 Wokhala ndi Woyang’anira Dera

‘Kulambira Mulungu Motsogoleredwa ndi Mzimu Komanso Coonadi’

Pulogilamu ya cigawo cam’mawa komanso camasana ya msonkhano wa dera wokhala ndi wa Dera.

Pezani Mayankho pa Mafunso Aya

Mafunsowa azayankhiwa mkati mwa pulogilamu.