Onani zimene zilipo

“Limba Mtima, Ugwile Nchitoyi Mwamphamvu”!

Kuti tilimbane na mavuto timafunika kudalila Yehova. Onani mmene zocita za Davide zinaonetsela kuti anali kudalila Mulungu.

Yacokela pa 1 Mbiri 28:1-20; 1 Samueli 16:1-23; 17:1-51

 

Mungakondenso Izi

NSANJA YA MLONDA

“Yehova Ndiye Mwini Nkhondo”

N’ciani cinathandiza Davide kugonjetsa Goliyati? Tingaphunzile ciani pa nkhani ya Davide?